Nyimbo ya Solomo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kodi mkazi+ amene akuchokera kuchipululuyu ndani,+ atakoloweka dzanja lake m’khosi mwa wachikondi wake?”+ “Ine ndinakudzutsa pansi pa mtengo wa maapozi. Pamenepo m’pamene mayi ako anamva zowawa pokubereka. Mayi amene anali kukubereka anamva zowawa ali pamenepo.+ Chivumbulutso 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+
5 “Kodi mkazi+ amene akuchokera kuchipululuyu ndani,+ atakoloweka dzanja lake m’khosi mwa wachikondi wake?”+ “Ine ndinakudzutsa pansi pa mtengo wa maapozi. Pamenepo m’pamene mayi ako anamva zowawa pokubereka. Mayi amene anali kukubereka anamva zowawa ali pamenepo.+
10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+