Miyambo 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yapha nyama yake ndipo yasakaniza vinyo wake. Kuwonjezera apo, yayala patebulo pake.+ Nyimbo ya Solomo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwenzi nditakutsogolera ndipo ndikanakulowetsa m’nyumba mwa mayi anga,+ amene ankandiphunzitsa. Ndikanakupatsa vinyo wothira zonunkhiritsa,+ ndi madzi a makangaza ongofinya kumene.
2 Bwenzi nditakutsogolera ndipo ndikanakulowetsa m’nyumba mwa mayi anga,+ amene ankandiphunzitsa. Ndikanakupatsa vinyo wothira zonunkhiritsa,+ ndi madzi a makangaza ongofinya kumene.