Nyimbo ya Solomo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dzuka, iwe mphepo yakumpoto. Bwera, iwe mphepo yakum’mwera.+ Womba pamunda wanga+ kuti kununkhira kwake kumveke.” “Wachikondi wanga alowe m’munda wake kuti adzadye zipatso zake zokoma kwambiri.”
16 Dzuka, iwe mphepo yakumpoto. Bwera, iwe mphepo yakum’mwera.+ Womba pamunda wanga+ kuti kununkhira kwake kumveke.” “Wachikondi wanga alowe m’munda wake kuti adzadye zipatso zake zokoma kwambiri.”