Nyimbo ya Solomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi+ ndiponso pali mphoyo+ zakutchire, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.+
7 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi+ ndiponso pali mphoyo+ zakutchire, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.+