Genesis 24:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Atatero, anafunsa mtumiki uja kuti: “Kodi munthu akubwera apoyo kuchokera m’tchire kudzakumana nafe ndani?” Mtumikiyo anayankha kuti: “Ameneyo ndi mbuyanga.” Pamenepo iye anatenga nsalu yophimba kumutu n’kudziphimba nayo.+
65 Atatero, anafunsa mtumiki uja kuti: “Kodi munthu akubwera apoyo kuchokera m’tchire kudzakumana nafe ndani?” Mtumikiyo anayankha kuti: “Ameneyo ndi mbuyanga.” Pamenepo iye anatenga nsalu yophimba kumutu n’kudziphimba nayo.+