Nyimbo ya Solomo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mpaka nthawi ya kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka, tembenuka wachikondi wanga. Ukhale ngati mbawala+ kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri amene akutilekanitsa.
17 Mpaka nthawi ya kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka, tembenuka wachikondi wanga. Ukhale ngati mbawala+ kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri amene akutilekanitsa.