Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+ Salimo 89:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira motonza,+Mmene atonzera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.+
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira motonza,+Mmene atonzera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.+