Ezekieli 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anandiyendetsa m’chigwamo kuti ndione mafupa onsewo. Ndinaona kuti m’chigwamo munali mafupa ambiri ndipo anali ouma kwambiri.+
2 Iye anandiyendetsa m’chigwamo kuti ndione mafupa onsewo. Ndinaona kuti m’chigwamo munali mafupa ambiri ndipo anali ouma kwambiri.+