Mika 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Oona masomphenya+ adzachita manyazi+ ndipo olosera+ adzakhumudwa ndithu. Onsewa adzaphimba ndevu zawo zapamlomo+ chifukwa Mulungu sadzawayankha.’”+
7 Oona masomphenya+ adzachita manyazi+ ndipo olosera+ adzakhumudwa ndithu. Onsewa adzaphimba ndevu zawo zapamlomo+ chifukwa Mulungu sadzawayankha.’”+