Mateyu 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amandipembedza pachabe, chifukwa amaphunzitsa malamulo a anthu ngati ziphunzitso za Mulungu.’”+ Maliko 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mumanyalanyaza malamulo a Mulungu, ndi kuumirira mwambo wa anthu.”+ Akolose 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinthu zimenezi zidzawonongedwa mwa kuzigwiritsa ntchito ndipo malamulo amenewa ndi ziphunzitso za anthu basi.+
22 Zinthu zimenezi zidzawonongedwa mwa kuzigwiritsa ntchito ndipo malamulo amenewa ndi ziphunzitso za anthu basi.+