Salimo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+