Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+ Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+ Aroma 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tikudziwa kuti Mulungu amaweruza anthu amene amachita zimenezi kuti ndi oyenera kulandira chilango ndipo chiweruzo chake ndi chogwirizana ndi choonadi.+
4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+
24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+
2 Tikudziwa kuti Mulungu amaweruza anthu amene amachita zimenezi kuti ndi oyenera kulandira chilango ndipo chiweruzo chake ndi chogwirizana ndi choonadi.+