Salimo 45:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana anu adzatenga+ malo a makolo anu,+Ndipo mudzawaika kukhala akalonga padziko lonse lapansi.+