Salimo 107:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lamchere,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo. Yesaya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+
6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+