Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+