Hoseya 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.
5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.