2 Mafumu 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi ungathe bwanji kubweza bwanamkubwa mmodzi, yemwe ndi mtumiki wotsika kwambiri wa mbuye wanga,+ pamene iweyo ukuchita kudalira Iguputo kuti akupatse magaleta+ ndi okwera pamahatchi?+ Yesaya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti iye adzanena kuti, ‘Kodi akalonga anga si mafumunso?+
24 Kodi ungathe bwanji kubweza bwanamkubwa mmodzi, yemwe ndi mtumiki wotsika kwambiri wa mbuye wanga,+ pamene iweyo ukuchita kudalira Iguputo kuti akupatse magaleta+ ndi okwera pamahatchi?+