2 Mafumu 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Senakeribu+ mfumu ya Asuri inachokako n’kubwerera+ kukakhala ku Ninive.+