2 Mafumu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti,+ ‘Ndamva pemphero+ limene wapemphera kwa ine lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+ Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti,+ ‘Ndamva pemphero+ limene wapemphera kwa ine lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+
1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+