2 Mafumu 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+ 2 Mbiri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+
34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+
22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+