Salimo 130:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+ Salimo 131:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndadzitonthoza ndipo ndakhazika mtima wanga pansi.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa, amene ali m’manja mwa mayi ake.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa.+
6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+
2 Ine ndadzitonthoza ndipo ndakhazika mtima wanga pansi.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa, amene ali m’manja mwa mayi ake.+Ndakhala ngati mwana amene wangosiya kumene kuyamwa.+