Salimo 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nanga tsopano, inu Yehova, ine ndikuyembekezera chiyani?Chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Salimo 119:82 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Maso anga alefuka chifukwa cholakalaka mawu anu,+Ndipo ndikunena kuti: “Kodi mudzandilimbikitsa liti?”+
82 Maso anga alefuka chifukwa cholakalaka mawu anu,+Ndipo ndikunena kuti: “Kodi mudzandilimbikitsa liti?”+