Salimo 63:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho ndidzakutamandani pa nthawi yonse ya moyo wanga.+Ndidzapemphera m’dzina lanu nditakweza manja anga.+ Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
4 Choncho ndidzakutamandani pa nthawi yonse ya moyo wanga.+Ndidzapemphera m’dzina lanu nditakweza manja anga.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+