2 Mafumu 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yesaya anati: “Amuna inu, tengani nkhuyu zouma zoumba pamodzi.”+ Choncho iwo anatenga nkhuyuzo n’kuziika pachithupsa+ chimene anali nacho, ndipo Hezekiya anachira pang’onopang’ono.+
7 Kenako Yesaya anati: “Amuna inu, tengani nkhuyu zouma zoumba pamodzi.”+ Choncho iwo anatenga nkhuyuzo n’kuziika pachithupsa+ chimene anali nacho, ndipo Hezekiya anachira pang’onopang’ono.+