Deuteronomo 28:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+ 2 Mafumu 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pambuyo pake mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.”
49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+
14 Pambuyo pake mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.”