Salimo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Phazi langa lidzaimadi pamalo athyathyathya.+Pamsonkhano, ndidzatamanda Yehova.+