Yobu 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi adzaphunzitsa Mulungu nzeru,+Pamene Mulunguyo azidzaweruza anthu apamwamba?+ Yobu 36:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndani wam’funsa kuti afotokoze za njira yake,+Ndipo ndani wamuuza kuti, ‘Mwachita zosalungama’?+ Aroma 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova,+ kapena ndani angakhale phungu wake?”+