Yesaya 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+
18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+