Salimo 103:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene akukukhutiritsa pa nthawi ya moyo wako ndi zinthu zabwino.+Mulungu akukuchititsa kukhalabe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+ Salimo 138:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku limene ine ndinaitana, inu munandiyankha.+Munandilimbitsa mtima ndi kundipatsa mphamvu.+
5 Amene akukukhutiritsa pa nthawi ya moyo wako ndi zinthu zabwino.+Mulungu akukuchititsa kukhalabe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+