Yobu 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nanga kuli bwanji munthu yemwe ndi mphutsi,Komanso mwana wa munthu yemwe ndi nyongolotsi?”+ Salimo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndine nyongolotsi+ osati munthu.Anthu amanditonza ndipo ndine wonyozeka kwa anthu.+