Salimo 107:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Amasandutsa chipululu kukhala dambo la madzi,+Ndipo dziko lopanda madzi amalisintha kukhala dera la akasupe amadzi.+
35 Amasandutsa chipululu kukhala dambo la madzi,+Ndipo dziko lopanda madzi amalisintha kukhala dera la akasupe amadzi.+