Salimo 89:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi imeneyo munalankhula ndi okhulupirika anu mwa masomphenya,+Ndipo munati:“Ndapereka thandizo kwa wamphamvu.+Ndakweza wosankhidwa mwapadera pakati pa anthu.+ Luka 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+ 1 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+
19 Pa nthawi imeneyo munalankhula ndi okhulupirika anu mwa masomphenya,+Ndipo munati:“Ndapereka thandizo kwa wamphamvu.+Ndakweza wosankhidwa mwapadera pakati pa anthu.+
35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+
4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+