Yobu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye amene moyo+ wa aliyense uli m’dzanja lake,Ndiponso mzimu wa anthu onse.+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+