Salimo 107:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu amene amayenda m’zombo panyanja,+Amene amachita malonda pamadzi ambiri,+