Yesaya 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “M’chipululumo mudzakhala chilungamo, ndiponso m’munda wa zipatsowo mudzakhala chilungamo.+ Yesaya 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chipululu ndi malo opanda madzi zidzasangalala.+ Dera lachipululu lidzakondwa ndipo lidzachita maluwa n’kukhala lokongola ngati duwa la safironi.+
35 Chipululu ndi malo opanda madzi zidzasangalala.+ Dera lachipululu lidzakondwa ndipo lidzachita maluwa n’kukhala lokongola ngati duwa la safironi.+