Yesaya 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ziyoni adzapulumutsidwa+ ndi chilungamo ndipo anthu ake amene adzabwerere, adzapulumutsidwanso ndi chilungamo.+ Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+ Yesaya 59:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Wowombolayo+ adzabwera ku Ziyoni+ ndiponso kwa mbadwa za Yakobo zimene zasiya zolakwa zawo,”+ akutero Yehova. 1 Akorinto 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+
27 Ziyoni adzapulumutsidwa+ ndi chilungamo ndipo anthu ake amene adzabwerere, adzapulumutsidwanso ndi chilungamo.+
20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
20 “Wowombolayo+ adzabwera ku Ziyoni+ ndiponso kwa mbadwa za Yakobo zimene zasiya zolakwa zawo,”+ akutero Yehova.
20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+