Yesaya 61:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzamanganso malo amene akhala owonongeka kwa nthawi yaitali.+ Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale.+ Adzakonzanso mizinda yowonongedwa,+ malo amene akhala osakazidwa ku mibadwomibadwo.
4 Iwo adzamanganso malo amene akhala owonongeka kwa nthawi yaitali.+ Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale.+ Adzakonzanso mizinda yowonongedwa,+ malo amene akhala osakazidwa ku mibadwomibadwo.