Yesaya 61:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+ 1 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ineyo ndinabzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndiye anakulitsa.+
11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+