Ezekieli 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu woipayo akaona+ zoipa zimene anali kuchita n’kuzisiya,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+
28 Munthu woipayo akaona+ zoipa zimene anali kuchita n’kuzisiya,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+