Ezekieli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene iwo anali kukhala pakati pawo,+ pakuti ndinawachititsa kuti andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo powatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Aroma 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.
9 Koma ine ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene iwo anali kukhala pakati pawo,+ pakuti ndinawachititsa kuti andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo powatulutsa m’dziko la Iguputo.+
24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.