Yesaya 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+