Yesaya 54:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+
2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+