Ekisodo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ana Aisiraeli anayenda panthaka youma pakati pa nyanja,+ ndipo madzi anaima ngati khoma kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+ Salimo 114:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyanja inaona ndipo inathawa.+Yorodano anabwerera m’mbuyo.+ Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+
29 Koma ana Aisiraeli anayenda panthaka youma pakati pa nyanja,+ ndipo madzi anaima ngati khoma kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+