Deuteronomo 28:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pakati pa mitundu imeneyo sudzakhala mwamtendere,+ ndipo sudzapeza malo oti phazi lako liponde kuti lipumulirepo. Kumeneko, Yehova adzakupatsa mtima wachinthenthe,+ adzachititsa maso ako+ khungu ndipo adzakutayitsa mtima. Yesaya 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khamu la mitundu yonse imene ikuchita nkhondo ndi Ariyeli,+ onse amene akumenyana naye ndi kumumangira nsanja zomenyerapo nkhondo, ndiponso amene akumukhwimitsira zinthu,+ adzaona ngati za m’maloto, za m’masomphenya a usiku.
65 Pakati pa mitundu imeneyo sudzakhala mwamtendere,+ ndipo sudzapeza malo oti phazi lako liponde kuti lipumulirepo. Kumeneko, Yehova adzakupatsa mtima wachinthenthe,+ adzachititsa maso ako+ khungu ndipo adzakutayitsa mtima.
7 Khamu la mitundu yonse imene ikuchita nkhondo ndi Ariyeli,+ onse amene akumenyana naye ndi kumumangira nsanja zomenyerapo nkhondo, ndiponso amene akumukhwimitsira zinthu,+ adzaona ngati za m’maloto, za m’masomphenya a usiku.