Yesaya 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pita, kaike mlonda pamalo ake, kuti anene zonse zimene aone.”+ Yesaya 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango,+ kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda, ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+
8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango,+ kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda, ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+