Yesaya 66:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Ululu wa pobereka usanamubwerere, iye anabereka mwana wamwamuna.+
7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Ululu wa pobereka usanamubwerere, iye anabereka mwana wamwamuna.+