Yesaya 58:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha inu, anthu adzamanga malo amene anawonongedwa kalekale.+ Inu mudzamanganso maziko amene akhalapo ku mibadwomibadwo.+ Mudzatchedwa otseka mipata ya mpanda,+ ndiponso okonzanso misewu yomwe anthu amakhala m’mphepete mwake.
12 Chifukwa cha inu, anthu adzamanga malo amene anawonongedwa kalekale.+ Inu mudzamanganso maziko amene akhalapo ku mibadwomibadwo.+ Mudzatchedwa otseka mipata ya mpanda,+ ndiponso okonzanso misewu yomwe anthu amakhala m’mphepete mwake.