Salimo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ofatsa adzadya ndi kukhuta.+Ofunafuna Yehova adzamutamanda.+Mitima yanu ikhale ndi moyo kosatha.+