Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+
11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+