Salimo 77:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke. Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke.
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?